У нас вы можете посмотреть бесплатно Iyi Ndi Nkhondo by The QFM или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Moyo wachikhristu ndi nkhondo ndi kuguba (battle and match). Pankhondo iyi mulibe kumasulidwa; kuyesetsa kukuyenera kukhala kosalekeza komanso kolimbikira. Ndi mwa kuyesetsa kosalekeza kuti tisungebe chigonjetso pa ziyeso za Satana. Umphumphu wachikristu uyenera kufunidwa ndi mphamvu zopanda malire ndi kusungidwa ndi cholinga chokhazikika. MH 453.2 Palibe amene adzakwezedwe mmwamba popanda khama ndi kulimbikira kwa iye yekha. Onse ayenera kuchita nawo nkhondoyi; palibe amene angamenye nkhondo zathu. Patokha tili ndi udindo pa nkhani zokhuzs kulimbana; Ngakhale kuti Nowa, Yobu, ndi Danieli anali m’dzikolo sakanatha kupulumutsa mwana wamwamuna kapena wamkazi mwa chilungamo chawo. MH 453.3