У нас вы можете посмотреть бесплатно BOMA LAKWIYA NDI NYERE (NYIMBO) YA DAN LU или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
BOMA LIKWIYA NDI NYIMBO YA DAN LU Nthambi yowona za luso (department of arts) ku Censorship Board yayankhula ndi woyimba wokhazikika mdziko muno Dan Lu pamodzi ndi katswiri wina wojambula nyimbo Tapps Bandawe pa nkhani yokhuza zina zomwe anayimba mu nyimbo yomwe yangotuluka kumene yotchedwa Take My Body. Nyimboyi yomwe ili ndi mawu olawula makamaka mu chiyankhulo chathu cha Chichewa yawusa mapiri pa chigwa mdziko muno pamene anthu ambiri akuwona kuti nyimboyo ndi yotukwana ndipo sikuyenera kunveredwa ndi anthu mdziko muno. Nyimboyi ikumayamba ndi mawu akuti mamuna ali ndi nyere ndipo akufuna kukhala pamodzi ndi mkazi wake.