У нас вы можете посмотреть бесплатно Estiner Katengeza - Zili Bwino (video) или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
We are blessed with so many good things. All we have to do is open our eyes and see it. Enjoy with the lyric below: Verse 1 Anayang'ana 'Mbuye wanga zonse analenga aaah Napepenyetsetsa Yehova, zonse anazilengaa aah Anayang'ana mbalame, Anayang'ana mitengo Zigwa ndi mitunda, nyama zosiyanasiyana aaah Anayang'ana munthu olengedwa m'chifaniziro chake, Ataona zonse 'Mbuye anati (zili bwino)x2 oh yey yey Chorus Anzanga mwandipatsa ndiyamika 'Mbuye wanga poti Ali bwino,, Abale mwandipatsa ndiyamika 'Mbuye wanga poti Ali bwino Makolo mwandipatsa ndiyamika 'Mbuye poti Ali bwino Dziko mwandipatsa ndiyamika mbuye wanga poti lili bwino, Zonse mwandipatsa ndiyamika 'Mbuye wanga poti (zili bwino)x2 oh yey yey Verse 2 Pamene mwandiika Ambuye ndikukuyamikani iii Kuti ndikwanilitse cholinga chanu ndikukuyamikani iii Nditumikire inu. Ndifikire mazana mazana: anzanga, abale, kunyumba, kusukulu, ngakhale ku ntchito oh oh Ndiwale monga munthu olengedwa m'chifaniziro chanu Poti mutalenga ine munati (ndili bwino)x2 oh yey yey (Chorus) Bridge (ah ah ah)x3 ah ah (ah ah ah)x3 ah ah (ah ah ah)x3 ah ah (ah ah ah)x3 ah ah (Chorus)