У нас вы можете посмотреть бесплатно ATOLANKHANI APANIKIZA MAFUSO NKULU WA MEC ANNABEL MTALIMANJA - MEC PRESS BRIEFING LILONGWE MALAWI или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Wapampando wa bungwe loyendetsa chisankho la MEC, Justice Annabel Mtalimanja watsimikiza kuti palibe munthu yemwe dzina lake linasowa kapena kufufutidwa mkaundula wa anthu odzaponya voti. A Mtalimanja ati, komishonala Francis Kasaila ndi anthu ena khumi, asanu ndi atatu (18) mayina awo analephera kusintha malo odzaponyera, koma MEC yakhazikitsa pa 15 April, ngati tsiku lomwe anthuwa adzasinthe malo odzaponya voti. A Mtalimanja atinso anthu 60,761 ndi omwe asintha malo odzaponya voti ndipo chiwerengero cha onse ndi 7, 216, 899. Iwo akulankhura pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe.