У нас вы можете посмотреть бесплатно Imfa yowawa yasataniki yodabwitsa Ya WalyCris Wanyengo или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
WOYIMBA WALYCRIS WAMWALIRA Woyimba wina yemwe watchuka kwambiri mdziko muno ndi nyimbo ya chiyankhulo cha chi Yao yotchedwa Achalume, Walycris, wamwalira kucha kwa lero pa 23 December 2022 pa ngozi yomwe bus yomwe anakwera ya Matours inagundana ndi truck. Bus yo imachokera mu mzinda wa Johannesburg mdziko la South Africa kubwera kuno ku Malawi ndipo inawombedwa ndi trailer ya truck yo ku mbali ya woyendetsa komwe kwavulala anthu angapo ndikupha Walycris. Malingana ndi malipoti, ngoziyi akuti yachitika pa malo ena otchedwa Ngundo omwe ali mdziko la Zimbabwe pa nthawi ya 3:20 ku m’bandakucha kwa lero pa 23 December 2022 ndipo truck yi akuti imayendetsedwa ndi driver yemwe akuganiziridwa kuti anali atalezera ndipo amagona. Bus yi akuti yangogulidwa kumene ndipo yatha mwezi umodzi wokha chibwelereni mdziko muno ndikuyamba ntchito yake yonyamula anthu pa msewu.