У нас вы можете посмотреть бесплатно WAKULA - CEN REE DON X FLEGOH или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Title :Wakula Artist: Cen ree Don x flegoh prod : on top records video by uncle P lyrics intro (flegoh x Cen ree Don) verse one(Cen ree Don) hello a friend paja inu ndi aBoss// simuphwekesa m'mapezeka ndima cross// chomwe ndikufuna ndingofuna imozi// ndizizimuse gulu by fire by force// usaphwekesetu iwe Anthony// ndingofuna zinthu zoti anthu andione// masten ndiye akundikalipira// akufuna mpongozi ati ine ndakula// Pena kuzifusa koma ine ndi munthu// kuumaku siza kumtundu// kapena ndikufunika JuJu// mayo mayo JuJu// X2 Pena kuzifusa koma ine ndi munthu// kuumaku siza kumtundu// kapena ndikufunika JuJu// mayo mayo JuJu// X2 Hook (Cen ree Don) Ndikangolakwa pang'ono Kwa masten ati Wakula ukwatire// ooh wooh wooh Ndimafuna cross undivungireko Mwina nane ndigwire// Nanga daily kumandikalipira kumandiraratira ati Wakula ukwatire// ndiyeno a friend ndatopa nazo Pena ngati ndilire// verse 2 ( flegoh) nawe pena ukunyanya ,ukunyanya ukutichitisa manyazi// ukuyenera ungomala basi ungomala nanga zoona kumasowa nkazi// olo mbiri ya mimba ,kutipanga ngati ndife otchipa// amzakofe man mumutriper ngati nkazi ndi uyo mumazimva // ahaaaah chabwino sankha-sankha uyu ndi bulenda koma kwawo nkwakachere // utha kumapenga pachibwezi pokha koma kubanja ndiye usakayese// chabwino sankhani-sankha uyu ndi bulenda koma kwawo nkwakachere // utha kumapenga pachibwezi pokha koma kubanja ndiye usakayese// Hook (Cen ree Don) Ndikangolakwa pang'ono Kwa masten ati Wakula ukwatire// ooh wooh wooh Ndimafuna cross undivungireko Mwina nane ndigwire// Nanga daily kumandikalipira kumandiraratira ati Wakula ukwatire// ndiyeno a friend ndatopa nazo Pena ngati ndilire//ooh wooh wooh