У нас вы можете посмотреть бесплатно Full Video Part 2 of Purple Sunday Mulungu Akalowa Munyengo Yako Nguluwe Wells of Life Assembly или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Malemba: Yohane 9:1–41 Bishop Banda analimbikitsa okhulupirira kuti akhale okhulupirika ndiponso asamachoke ku tchalitchi chimodzi chimene Mulungu waika, ndipo atumikire Mulungu mokhulupirika. Mawu ake ofunika anali awa: Dalitso la Mulungu limasintha moyo ndipo anthu ena sangamvetse momwe zaterera. Tikayima pa choonadi, Mulungu nayenso azayima nafe, ngakhale titakumana ndi mavuto. Monga Danieli m’dzenje la mikango, Mulungu anaima naye, komanso azayima nafe m’mavuto athu. Alipo madalitso ena amene anthu sadzamvetsa momwe zaterera pa moyo wathu. Kulimbikira moyo wauzimu n’kofunika ngakhale zitatheka kuti tisiye abwenzi ena. Yesu amamva komanso amaona zonse zomwe tikukumana nazo – amasamalira ife. Kwa amene anakana ndi anthu, Yesu Khristu ndi pothawira komanso amathandiza ndi kulimbikitsa. Zina mwa mavuto amene tikukumana nawo zimachitika chifukwa cha kusamvela