У нас вы можете посмотреть бесплатно APM Munalephela Kufufuza Imfa Ya Bingu Lero Muzitinamiza Kuti Mufufuza Za Chilima Yusuf Jonas или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
On Nyasa VoiceBox, Yusuf Jonas says he is doubtful that APM will conduct an honest inquiry into the death of Vice President Saulos Chilima. He argues that APM previously claimed that his brother, the late President Bingu wa Mutharika, was poisoned but did not pursue an investigation into the matter. He questions how someone who failed to investigate his own brother’s death during his presidency from 2014 to 2020 can now be expected to properly inquire into Chilima’s death. Ku Nyasa Voicebox, Yusuf Jonas wati akukayika kuti APM angafufuze moona mtima za imfa ya Vice President Saulos Chilima. Iye wati APM adanenapo kale kuti mchimwene wake, malemu Purezidenti Bingu wa Mutharika adadyedwa ndi poizoni koma sadachite kafukufuku pankhaniyi. Iye akufunsa momwe munthu yemwe adalephera kufufuza za imfa ya mchimwene wake yemwe adamwalira kuyambira 2014 mpaka 2020 tsopano akuyembekezeka kufufuza bwino za imfa ya Chilima. #malawi