У нас вы можете посмотреть бесплатно LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021 или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Banja la a Banda likukumana ndi mavuto pamene anthu angapo akudwala. Lucius Banda wakhala akudwala matenda a impsyo kuyambila December 2020 ndipo wagonekedwa ku chipatala kuno ku Malawi komanso ku South Africa kwa masabata 6. Pano akulandira chilandiro cha dialysis ku Mwaiwathu Hospital. Mchimwene wake Sir Paul Banda naye akudwala matenda a impsyo omwewo ndipo akufunika akalandire impsyo ina ku India. Izi zikufunika ndalama zosachepela 30 million kwacha. Mu banja momwemo, Francis, mkulu wake wa Lucius (mng'ono wa Paul) akudwala cancer yotchedwa leukemia ndipo akulandira chemotherapy. Izi zapangitsa banjali kugwilitsa ntchito ndalama zochuluka ndipo anthu akufuna kwabwino akhala akusonkha ndalama kuti awathandize.