У нас вы можете посмотреть бесплатно Kodi Chili ndi Phindu Lalikulu kwambiri Kumwamba ndi chiyani? | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu или скачать в максимальном доступном качестве, видео которое было загружено на ютуб. Для загрузки выберите вариант из формы ниже:
Если кнопки скачивания не
загрузились
НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием видео, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу
страницы.
Спасибо за использование сервиса ClipSaver.ru
Kodi Tingapeze kuti Moyo Wofunika Kwambiri Umene Tidzakhala Kosatha? Kudzera m’Baibulo, Mulungu adatiphunzitsa momwe tingakhalire moyo wamtengo wapata womwe umatilola ife kulandira ulemerero wa Kumwamba. Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi Atidzwitsa Phindu la Kumwamba Monga madzi ndi ofunika kwambiri kuposa golide woyenga bwino mu chipululu ndi m’busa ndi ofunika kwambiri kuposa mfumu kwa nkhosa yosochera, ziwalo za Mpingo wa Mulungu, amalemekeza ziphunzitso za Pangano Latsopano monga Sabata ndi Paska,zomwe zitha kutsogolera ife ku Ufumu Wakumwamba.. [Ahebri 9:27–28] Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro; kotero Khristunso . . . adzaonekera pa nthawi yachiwiri, wopanda uchimo, kwa iwo amene amlindirira, kufikira chipulumutso. [Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.] 〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org 〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny 〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com